Quran with Chichewa translation - Surah An-Najm ayat 45 - النَّجم - Page - Juz 27
﴿وَأَنَّهُۥ خَلَقَ ٱلزَّوۡجَيۡنِ ٱلذَّكَرَ وَٱلۡأُنثَىٰ ﴾
[النَّجم: 45]
﴿وأنه خلق الزوجين الذكر والأنثى﴾ [النَّجم: 45]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo Iye ndiAmene adalenga mitundu iwiri: chachimuna ndi chachikazi, (anthu ndi zamoyo zina) |