Quran with Chichewa translation - Surah Al-Muddaththir ayat 50 - المُدثر - Page - Juz 29
﴿كَأَنَّهُمۡ حُمُرٞ مُّسۡتَنفِرَةٞ ﴾
[المُدثر: 50]
﴿كأنهم حمر مستنفرة﴾ [المُدثر: 50]
Khaled Ibrahim Betala “(Akuyenda mothamanga kuti asamve chenjezoli) ngati kuti iwo ndi mbidzi zothawa |