Quran with Chichewa translation - Surah Al-hijr ayat 76 - الحِجر - Page - Juz 14
﴿وَإِنَّهَا لَبِسَبِيلٖ مُّقِيمٍ ﴾
[الحِجر: 76]
﴿وإنها لبسبيل مقيم﴾ [الحِجر: 76]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo (midzi) iyi (yomwe tidaiwononga chotereyi), ili chikhalire m’njira moyenda anthu (ndipo iwo akuona zizindikiro zake) |