×

Iwo adatsatira zimene a Satana adanena mu Ufumu wa Solomoni. Sikuti Solomoni 2:102 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:102) ayat 102 in Chichewa

2:102 Surah Al-Baqarah ayat 102 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 102 - البَقَرَة - Page - Juz 1

﴿وَٱتَّبَعُواْ مَا تَتۡلُواْ ٱلشَّيَٰطِينُ عَلَىٰ مُلۡكِ سُلَيۡمَٰنَۖ وَمَا كَفَرَ سُلَيۡمَٰنُ وَلَٰكِنَّ ٱلشَّيَٰطِينَ كَفَرُواْ يُعَلِّمُونَ ٱلنَّاسَ ٱلسِّحۡرَ وَمَآ أُنزِلَ عَلَى ٱلۡمَلَكَيۡنِ بِبَابِلَ هَٰرُوتَ وَمَٰرُوتَۚ وَمَا يُعَلِّمَانِ مِنۡ أَحَدٍ حَتَّىٰ يَقُولَآ إِنَّمَا نَحۡنُ فِتۡنَةٞ فَلَا تَكۡفُرۡۖ فَيَتَعَلَّمُونَ مِنۡهُمَا مَا يُفَرِّقُونَ بِهِۦ بَيۡنَ ٱلۡمَرۡءِ وَزَوۡجِهِۦۚ وَمَا هُم بِضَآرِّينَ بِهِۦ مِنۡ أَحَدٍ إِلَّا بِإِذۡنِ ٱللَّهِۚ وَيَتَعَلَّمُونَ مَا يَضُرُّهُمۡ وَلَا يَنفَعُهُمۡۚ وَلَقَدۡ عَلِمُواْ لَمَنِ ٱشۡتَرَىٰهُ مَا لَهُۥ فِي ٱلۡأٓخِرَةِ مِنۡ خَلَٰقٖۚ وَلَبِئۡسَ مَا شَرَوۡاْ بِهِۦٓ أَنفُسَهُمۡۚ لَوۡ كَانُواْ يَعۡلَمُونَ ﴾
[البَقَرَة: 102]

Iwo adatsatira zimene a Satana adanena mu Ufumu wa Solomoni. Sikuti Solomoni sadakhulupirire ai koma a Satana ndiwo sadakhulupirire. Iwo amaphunzitsa anthu matsenga ndi zimene zidavumbulutsidwa kwa angelo awiri Harut ndi Marut ku Babuloni. Koma iwo samaphunzitsa wina aliyense mpaka atanena kuti: “Ndithudi ife tili kukuyesani inu, ndipo musakhale wosakhulupirira ayi.” Kuchokera kwa angelo chimene chimamasula pakati pa mwamuna ndi mkazi wake, ndipo iwo sadaononge wina aliyense ndi zimene adaphunzira kupatula ndi chilolezo cha Mulungu. Iwo amaphunzira zinthu zimene zimawaononga ndipo sizidawapindulire china chilichonse. Ndithudi iwo amadziwa kuti aliyense amene amachita matsenga sadzakhala ndi gawo m’moyo umene uli nkudza. Zopanda pake ndi zimene agulitsa nazo moyo wawo, iwo akadadziwa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: واتبعوا ما تتلوا الشياطين على ملك سليمان وما كفر سليمان ولكن الشياطين, باللغة نيانجا

﴿واتبعوا ما تتلوا الشياطين على ملك سليمان وما كفر سليمان ولكن الشياطين﴾ [البَقَرَة: 102]

❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek