Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 147 - البَقَرَة - Page - Juz 2
﴿ٱلۡحَقُّ مِن رَّبِّكَ فَلَا تَكُونَنَّ مِنَ ٱلۡمُمۡتَرِينَ ﴾ 
[البَقَرَة: 147]
﴿الحق من ربك فلا تكونن من الممترين﴾ [البَقَرَة: 147]
| Khaled Ibrahim Betala “(Kuyang’ana ku Al-Kaaba popemphera Swala ndicho) choonadi chomwe chachokera kwa Mbuye wako, choncho usakhale mmodzi mwa openekera |