×

Mtundu uli wonse uli ndi mbali imene umayang’ana popemphera. Motero limbikirani pochita 2:148 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:148) ayat 148 in Chichewa

2:148 Surah Al-Baqarah ayat 148 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 148 - البَقَرَة - Page - Juz 2

﴿وَلِكُلّٖ وِجۡهَةٌ هُوَ مُوَلِّيهَاۖ فَٱسۡتَبِقُواْ ٱلۡخَيۡرَٰتِۚ أَيۡنَ مَا تَكُونُواْ يَأۡتِ بِكُمُ ٱللَّهُ جَمِيعًاۚ إِنَّ ٱللَّهَ عَلَىٰ كُلِّ شَيۡءٖ قَدِيرٞ ﴾
[البَقَرَة: 148]

Mtundu uli wonse uli ndi mbali imene umayang’ana popemphera. Motero limbikirani pochita zabwino. Kulikonse kumene mudzakhale, Mulungu adzakusonkhanitsani pamodzi. Ndithudi Mulungu ali ndi mphamvu pa chinthu china chilichonse

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولكل وجهة هو موليها فاستبقوا الخيرات أين ما تكونوا يأت بكم الله, باللغة نيانجا

﴿ولكل وجهة هو موليها فاستبقوا الخيرات أين ما تكونوا يأت بكم الله﴾ [البَقَرَة: 148]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo (mpingo) uliwonse udali ndi chibula chimene udali kuchilunjika. Choncho pikisanani pochita zabwino. Paliponse pamene mungakhale Allah adzakubweretsani nonsenu pamodzi (pa tsiku la chimaliziro). Ndithudi, Allah Ngokhoza chinthu chilichonse
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek