Quran with Chichewa translation - Surah Ta-Ha ayat 13 - طه - Page - Juz 16
﴿وَأَنَا ٱخۡتَرۡتُكَ فَٱسۡتَمِعۡ لِمَا يُوحَىٰٓ ﴾
[طه: 13]
﴿وأنا اخترتك فاستمع لما يوحى﴾ [طه: 13]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo Ine ndakusankha (kuti ukhale Mtumiki); choncho mvera zonse zomwe zikuvumbulutsidwa (kwa iwe) |