Quran with Chichewa translation - Surah Ash-Shu‘ara’ ayat 36 - الشعراء - Page - Juz 19
﴿قَالُوٓاْ أَرۡجِهۡ وَأَخَاهُ وَٱبۡعَثۡ فِي ٱلۡمَدَآئِنِ حَٰشِرِينَ ﴾
[الشعراء: 36]
﴿قالوا أرجه وأخاه وابعث في المدائن حاشرين﴾ [الشعراء: 36]
Khaled Ibrahim Betala “(Anthu) adati (kwa Farawo): “Mpatse nthawi ndi m’bale wakeyo, ndipo tumiza (amithenga) m’mizinda yonse osonkhanitsa anthu.” |