Quran with Chichewa translation - Surah Ash-Shu‘ara’ ayat 65 - الشعراء - Page - Juz 19
﴿وَأَنجَيۡنَا مُوسَىٰ وَمَن مَّعَهُۥٓ أَجۡمَعِينَ ﴾
[الشعراء: 65]
﴿وأنجينا موسى ومن معه أجمعين﴾ [الشعراء: 65]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo tidapulumutsa Mûsa ndi onse amene adali nawo (mpaka adaoloka nyanjayo, madzi ali chiimire mbali iyi ndi iyi) |