×

Kodi munthu amene atsata zokondweretsa Mulungu angafanizidwe ndi munthu amene walandira mkwiyo 3:162 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah al-‘Imran ⮕ (3:162) ayat 162 in Chichewa

3:162 Surah al-‘Imran ayat 162 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah al-‘Imran ayat 162 - آل عِمران - Page - Juz 4

﴿أَفَمَنِ ٱتَّبَعَ رِضۡوَٰنَ ٱللَّهِ كَمَنۢ بَآءَ بِسَخَطٖ مِّنَ ٱللَّهِ وَمَأۡوَىٰهُ جَهَنَّمُۖ وَبِئۡسَ ٱلۡمَصِيرُ ﴾
[آل عِمران: 162]

Kodi munthu amene atsata zokondweretsa Mulungu angafanizidwe ndi munthu amene walandira mkwiyo wa Mulungu? Gahena idzakhala mudzi wake ndipo malo omwe adzakhalako ndi onyansa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: أفمن اتبع رضوان الله كمن باء بسخط من الله ومأواه جهنم وبئس, باللغة نيانجا

﴿أفمن اتبع رضوان الله كمن باء بسخط من الله ومأواه جهنم وبئس﴾ [آل عِمران: 162]

Khaled Ibrahim Betala
“Kodi amene akutsata chokondweretsa Allah angalingane ndi yemwe wabwerera ndi mkwiyo wochokera kwa Allah, ndipo Jahannam nkukhala malo ake? Taonani kuipa kumalo obwerera
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek