Quran with Chichewa translation - Surah As-saffat ayat 63 - الصَّافَات - Page - Juz 23
﴿إِنَّا جَعَلۡنَٰهَا فِتۡنَةٗ لِّلظَّٰلِمِينَ ﴾
[الصَّافَات: 63]
﴿إنا جعلناها فتنة للظالمين﴾ [الصَّافَات: 63]
Khaled Ibrahim Betala “Ndithu Ife taupanga (mtengo umenewu) kukhala mayeso ndi chilango cha anthu ochimwa (podzichitira okha chinyengo ndi kupembedza mafano) |