Quran with Chichewa translation - Surah Al-Fath ayat 28 - الفَتح - Page - Juz 26
﴿هُوَ ٱلَّذِيٓ أَرۡسَلَ رَسُولَهُۥ بِٱلۡهُدَىٰ وَدِينِ ٱلۡحَقِّ لِيُظۡهِرَهُۥ عَلَى ٱلدِّينِ كُلِّهِۦۚ وَكَفَىٰ بِٱللَّهِ شَهِيدٗا ﴾
[الفَتح: 28]
﴿هو الذي أرسل رسوله بالهدى ودين الحق ليظهره على الدين كله وكفى﴾ [الفَتح: 28]
Khaled Ibrahim Betala “Iye ndi Yemwe adatumiza Mtumiki Wake ndi chiongoko ndi chipembedzo choona kuti achiike pamwamba pa zipembedzo zonse. Ndipo Allah akukwanira kukhala mboni (yake) |