Quran with Chichewa translation - Surah Al-hashr ayat 1 - الحَشر - Page - Juz 28
﴿سَبَّحَ لِلَّهِ مَا فِي ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَمَا فِي ٱلۡأَرۡضِۖ وَهُوَ ٱلۡعَزِيزُ ٱلۡحَكِيمُ ﴾
[الحَشر: 1]
﴿سبح لله ما في السموات وما في الأرض وهو العزيز الحكيم﴾ [الحَشر: 1]
Khaled Ibrahim Betala “Zonse za kumwamba ndi za pansi zimalemekeza Allah (ndi kumuyeretsa ku khalidwe losayenera ndi ulemelero Wake). Ndipo Iye Ngopambana (salephera kanthu), Ngwaluntha (m’kakonzedwe Kake ndi m’zochita Zake) |