Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 68 - الأعرَاف - Page - Juz 8
﴿أُبَلِّغُكُمۡ رِسَٰلَٰتِ رَبِّي وَأَنَا۠ لَكُمۡ نَاصِحٌ أَمِينٌ ﴾
[الأعرَاف: 68]
﴿أبلغكم رسالات ربي وأنا لكم ناصح أمين﴾ [الأعرَاف: 68]
Khaled Ibrahim Betala ““Ndikufikitsa kwa inu uthenga wa Mbuye wanga. Ndipo ine ndine mlangizi wanu (wokufunirani zabwino), wokhulupirika.” |