Quran with Chichewa translation - Surah At-Takwir ayat 14 - التَّكوير - Page - Juz 30
﴿عَلِمَتۡ نَفۡسٞ مَّآ أَحۡضَرَتۡ ﴾
[التَّكوير: 14]
﴿علمت نفس ما أحضرت﴾ [التَّكوير: 14]
Khaled Ibrahim Betala “(Zikadzachitika zimenezi) mzimu uliwonse udzadziwa zimene wabweretsa (zabwino ndi zoipa) |