Quran with Chichewa translation - Surah Al-Fajr ayat 10 - الفَجر - Page - Juz 30
﴿وَفِرۡعَوۡنَ ذِي ٱلۡأَوۡتَادِ ﴾
[الفَجر: 10]
﴿وفرعون ذي الأوتاد﴾ [الفَجر: 10]
Khaled Ibrahim Betala “Komanso Firiauna (Farawo) mwini magulu ankhondo (omwe amalimbikitsa ufumu wake monga momwe zichiri zimalimbikitsira tenti) |