Quran with Chichewa translation - Surah Al-Fajr ayat 9 - الفَجر - Page - Juz 30
﴿وَثَمُودَ ٱلَّذِينَ جَابُواْ ٱلصَّخۡرَ بِٱلۡوَادِ ﴾
[الفَجر: 9]
﴿وثمود الذين جابوا الصخر بالواد﴾ [الفَجر: 9]
Khaled Ibrahim Betala “Ndi Asamudu, (anthu a mneneri Swaleh) amene adali kudula matanthwe ku chigwa (chotchedwa Wadi Qura ndi kumamanga nyumba zikuluzikulu) |