Quran with Chichewa translation - Surah Al-Fajr ayat 14 - الفَجر - Page - Juz 30
﴿إِنَّ رَبَّكَ لَبِٱلۡمِرۡصَادِ ﴾
[الفَجر: 14]
﴿إن ربك لبالمرصاد﴾ [الفَجر: 14]
Khaled Ibrahim Betala “Ndithu Mbuye wako ali tcheru (ndi zochita za anthu. Ndipo akuwasungira kuti adzawalipire) |