Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 93 - التوبَة - Page - Juz 10
﴿۞ إِنَّمَا ٱلسَّبِيلُ عَلَى ٱلَّذِينَ يَسۡتَـٔۡذِنُونَكَ وَهُمۡ أَغۡنِيَآءُۚ رَضُواْ بِأَن يَكُونُواْ مَعَ ٱلۡخَوَالِفِ وَطَبَعَ ٱللَّهُ عَلَىٰ قُلُوبِهِمۡ فَهُمۡ لَا يَعۡلَمُونَ ﴾
[التوبَة: 93]
﴿إنما السبيل على الذين يستأذنونك وهم أغنياء رضوا بأن يكونوا مع الخوالف﴾ [التوبَة: 93]
Khaled Ibrahim Betala “۞ Ndithu njira (yodzudzulidwa) ili pa arnene akukupempha chilolezo (choti asapite ku nkhondo ndi kusiyanso kupereka chuma chawo) pomwe iwo ngolemera. Akonda kukhala pamodzi ndi otsala m’mbuyo. Ndipo Allah wadinda chidindo (cha mantha) m’mitima mwawo, tero sadziwa (chilichonse chowathandiza) |