Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 94 - التوبَة - Page - Juz 11
﴿يَعۡتَذِرُونَ إِلَيۡكُمۡ إِذَا رَجَعۡتُمۡ إِلَيۡهِمۡۚ قُل لَّا تَعۡتَذِرُواْ لَن نُّؤۡمِنَ لَكُمۡ قَدۡ نَبَّأَنَا ٱللَّهُ مِنۡ أَخۡبَارِكُمۡۚ وَسَيَرَى ٱللَّهُ عَمَلَكُمۡ وَرَسُولُهُۥ ثُمَّ تُرَدُّونَ إِلَىٰ عَٰلِمِ ٱلۡغَيۡبِ وَٱلشَّهَٰدَةِ فَيُنَبِّئُكُم بِمَا كُنتُمۡ تَعۡمَلُونَ ﴾
[التوبَة: 94]
﴿يعتذرون إليكم إذا رجعتم إليهم قل لا تعتذروا لن نؤمن لكم قد﴾ [التوبَة: 94]
Khaled Ibrahim Betala “Akudandaulirani madandaulo mukabwerera kwa iwo (ndi kukumana nawo). Nena: “Musapereke madandaulo; sitikukhulupirirani. Allah watifotokozera kale nkhani zanu. Posachedwa Allah ndi Mtumiki Wake aona zochita zanu, kenako muzabwezedwa (pambuyo pa imfa) kwa Wodziwa zamseri ndi zoonekera. Choncho, Iye adzakufotokozerani zimene mudali kuchita.” |