×

Pambuyo pake tinawapulumutsa Atumwi athu pamodzi ndi amene amakhulupirira. Kotero ndi koyenera 10:103 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Yunus ⮕ (10:103) ayat 103 in Chichewa

10:103 Surah Yunus ayat 103 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Yunus ayat 103 - يُونس - Page - Juz 11

﴿ثُمَّ نُنَجِّي رُسُلَنَا وَٱلَّذِينَ ءَامَنُواْۚ كَذَٰلِكَ حَقًّا عَلَيۡنَا نُنجِ ٱلۡمُؤۡمِنِينَ ﴾
[يُونس: 103]

Pambuyo pake tinawapulumutsa Atumwi athu pamodzi ndi amene amakhulupirira. Kotero ndi koyenera kwa Ife kupulumutsa anthu okhulupirira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ثم ننجي رسلنا والذين آمنوا كذلك حقا علينا ننج المؤمنين, باللغة نيانجا

﴿ثم ننجي رسلنا والذين آمنوا كذلك حقا علينا ننج المؤمنين﴾ [يُونس: 103]

Khaled Ibrahim Betala
“Kenako tidzawapulumutsa atumiki Athu ndi amene adakhulupirira. Chotere nkoyenera kwa Ife kuwapulumutsa okhulupirira
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek