Quran with Chichewa translation - Surah Al-Humazah ayat 3 - الهُمَزة - Page - Juz 30
﴿يَحۡسَبُ أَنَّ مَالَهُۥٓ أَخۡلَدَهُۥ ﴾
[الهُمَزة: 3]
﴿يحسب أن ماله أخلده﴾ [الهُمَزة: 3]
Khaled Ibrahim Betala “Akuganiza kuti chuma chakecho chimkhazika (pa dziko) nthawi yaitali (ndikumteteza ku zimene sakuzifuna) |