Quran with Chichewa translation - Surah Al-Masad ayat 4 - المَسَد - Page - Juz 30
﴿وَٱمۡرَأَتُهُۥ حَمَّالَةَ ٱلۡحَطَبِ ﴾
[المَسَد: 4]
﴿وامرأته حمالة الحطب﴾ [المَسَد: 4]
Khaled Ibrahim Betala “Nayenso mkazi wake (adzalowa ku Moto) yemwe adali kusenza nkhuni (za minga pomutchera Mtumiki (s.a.w) komanso amanka nadanitsa pakati pa anthu |