Quran with Chichewa translation - Surah Ar-Ra‘d ayat 19 - الرَّعد - Page - Juz 13
﴿۞ أَفَمَن يَعۡلَمُ أَنَّمَآ أُنزِلَ إِلَيۡكَ مِن رَّبِّكَ ٱلۡحَقُّ كَمَنۡ هُوَ أَعۡمَىٰٓۚ إِنَّمَا يَتَذَكَّرُ أُوْلُواْ ٱلۡأَلۡبَٰبِ ﴾
[الرَّعد: 19]
﴿أفمن يعلم أنما أنـزل إليك من ربك الحق كمن هو أعمى إنما﴾ [الرَّعد: 19]
Khaled Ibrahim Betala “Kodi amene akudziwa kuti zimene zavumbulutsidwa kwa iwe kuchokera kwa Mbuye wako nzoona, angafanane ndi yemwe ali wakhungu? Ndithudi eni nzeru ndi okhawo olingalira |