×

“Motero choka ndi abale ako pakati pa usiku, iwe uziyenda pambuyo pawo 15:65 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-hijr ⮕ (15:65) ayat 65 in Chichewa

15:65 Surah Al-hijr ayat 65 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-hijr ayat 65 - الحِجر - Page - Juz 14

﴿فَأَسۡرِ بِأَهۡلِكَ بِقِطۡعٖ مِّنَ ٱلَّيۡلِ وَٱتَّبِعۡ أَدۡبَٰرَهُمۡ وَلَا يَلۡتَفِتۡ مِنكُمۡ أَحَدٞ وَٱمۡضُواْ حَيۡثُ تُؤۡمَرُونَ ﴾
[الحِجر: 65]

“Motero choka ndi abale ako pakati pa usiku, iwe uziyenda pambuyo pawo ndipo usalole wina aliyense kuti atembenuke. Kapita kumene walamulidwa kupita.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فأسر بأهلك بقطع من الليل واتبع أدبارهم ولا يلتفت منكم أحد وامضوا, باللغة نيانجا

﴿فأسر بأهلك بقطع من الليل واتبع أدبارهم ولا يلتفت منكم أحد وامضوا﴾ [الحِجر: 65]

Khaled Ibrahim Betala
““Choncho, choka ndi banja lako mkati mwa usiku; ndipo iwe udziwatsata pambuyo pawo; tsono aliyense wa inu asayang’ane kumbuyo (akamva mkokomo wachilango chochokera kumwamba, kuopa kuti angafe), ndipo yendani (mwachangu) kunka komwe mukulamulidwa.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek