×

Iye adakulengerani nyama ndipo mu izo mumapeza zofunda ndi zithandizo zina ndiponso 16:5 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nahl ⮕ (16:5) ayat 5 in Chichewa

16:5 Surah An-Nahl ayat 5 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nahl ayat 5 - النَّحل - Page - Juz 14

﴿وَٱلۡأَنۡعَٰمَ خَلَقَهَاۖ لَكُمۡ فِيهَا دِفۡءٞ وَمَنَٰفِعُ وَمِنۡهَا تَأۡكُلُونَ ﴾
[النَّحل: 5]

Iye adakulengerani nyama ndipo mu izo mumapeza zofunda ndi zithandizo zina ndiponso nyamazo mumadya

❮ Previous Next ❯

ترجمة: والأنعام خلقها لكم فيها دفء ومنافع ومنها تأكلون, باللغة نيانجا

﴿والأنعام خلقها لكم فيها دفء ومنافع ومنها تأكلون﴾ [النَّحل: 5]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo adalenga ziweto (monga ngamira, ng’ombe ndi mbuzi) mwa izo mukupeza zofunda, ndi zothandiza (zina zambiri), ndipo zina mwa izo mumazidya
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek