×

Ndipo mumanyadira pamene mumazisaka kudza nazo ku nyumba kwanu madzulo ndi pamene 16:6 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nahl ⮕ (16:6) ayat 6 in Chichewa

16:6 Surah An-Nahl ayat 6 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nahl ayat 6 - النَّحل - Page - Juz 14

﴿وَلَكُمۡ فِيهَا جَمَالٌ حِينَ تُرِيحُونَ وَحِينَ تَسۡرَحُونَ ﴾
[النَّحل: 6]

Ndipo mumanyadira pamene mumazisaka kudza nazo ku nyumba kwanu madzulo ndi pamene mumapita nazo kuubusa kukazidyetsa m’mawa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولكم فيها جمال حين تريحون وحين تسرحون, باللغة نيانجا

﴿ولكم فيها جمال حين تريحون وحين تسرحون﴾ [النَّحل: 6]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo mumakondwa ndi kunyadira chifukwa cha kukongola kwa izo mukamabwera nazo (kuchokera kubusa mimba zitakhuta), ndi popita nazo (kubusa zikuyenda mwandawala)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek