Quran with Chichewa translation - Surah Maryam ayat 33 - مَريَم - Page - Juz 16
﴿وَٱلسَّلَٰمُ عَلَيَّ يَوۡمَ وُلِدتُّ وَيَوۡمَ أَمُوتُ وَيَوۡمَ أُبۡعَثُ حَيّٗا ﴾
[مَريَم: 33]
﴿والسلام علي يوم ولدت ويوم أموت ويوم أبعث حيا﴾ [مَريَم: 33]
Khaled Ibrahim Betala ““Ndipo mtendere uli pa ine kuyambira tsiku lomwe ndidabadwa ndi tsiku limene ndidzamwalira, ndi tsiku limene ndidzaukitsidwa (kwa akufa tsiku la chiweruziro) ndikukhala ndi moyo.” |