×

Mulungu ndiye Mwini wake wa ku m’mawa ndi ku madzulo, motero mbali 2:115 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:115) ayat 115 in Chichewa

2:115 Surah Al-Baqarah ayat 115 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 115 - البَقَرَة - Page - Juz 1

﴿وَلِلَّهِ ٱلۡمَشۡرِقُ وَٱلۡمَغۡرِبُۚ فَأَيۡنَمَا تُوَلُّواْ فَثَمَّ وَجۡهُ ٱللَّهِۚ إِنَّ ٱللَّهَ وَٰسِعٌ عَلِيمٞ ﴾
[البَقَرَة: 115]

Mulungu ndiye Mwini wake wa ku m’mawa ndi ku madzulo, motero mbali iliyonse imene muyang’ana kuli Mulungu. Ndithudi Iye ndi okwana pa zofuna za zolengedwa zake ndipo Iye amadziwa china chilichonse

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولله المشرق والمغرب فأينما تولوا فثم وجه الله إن الله واسع عليم, باللغة نيانجا

﴿ولله المشرق والمغرب فأينما تولوا فثم وجه الله إن الله واسع عليم﴾ [البَقَرَة: 115]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo kuvuma ndi kuzambwe nkwa Allah; ndipo pamalo paliponse pamene mwatembenukira, (pomwe Allah wakulamulirani kuti mutembenukire), pamenepo mupezapo chiyanjo cha Allah. Ndithudi Allah Ngokwanira ponseponse, Wodziwa chilichonse
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek