×

“Oh Ambuye wathu! Atumizireni Mtumwi kuchokera kumtundu wawo amene adzawawerengera Mawu Anu 2:129 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:129) ayat 129 in Chichewa

2:129 Surah Al-Baqarah ayat 129 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 129 - البَقَرَة - Page - Juz 1

﴿رَبَّنَا وَٱبۡعَثۡ فِيهِمۡ رَسُولٗا مِّنۡهُمۡ يَتۡلُواْ عَلَيۡهِمۡ ءَايَٰتِكَ وَيُعَلِّمُهُمُ ٱلۡكِتَٰبَ وَٱلۡحِكۡمَةَ وَيُزَكِّيهِمۡۖ إِنَّكَ أَنتَ ٱلۡعَزِيزُ ٱلۡحَكِيمُ ﴾
[البَقَرَة: 129]

“Oh Ambuye wathu! Atumizireni Mtumwi kuchokera kumtundu wawo amene adzawawerengera Mawu Anu ndi kuwaphunzitsa Buku ndiponso luntha ndi kuwayeretsa iwo ku machimo awo. Ndithudi Inu ndinu Mwini mphamvu zonse ndi Mwini nzeru zonse.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ربنا وابعث فيهم رسولا منهم يتلو عليهم آياتك ويعلمهم الكتاب والحكمة ويزكيهم, باللغة نيانجا

﴿ربنا وابعث فيهم رسولا منهم يتلو عليهم آياتك ويعلمهم الكتاب والحكمة ويزكيهم﴾ [البَقَرَة: 129]

Khaled Ibrahim Betala
““E Mbuye wathu! Atumizireni mtumiki wochokera mwa iwo, kuti awawerengere Ayah (ndime) zanu ndikuwaphunzitsa buku (Lanu) ndi nzeru ndikuti awayeretse. Ndithudi Inu Ndinu Amphamvu zoposa, Anzeru zakuya.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek