×

“Ambuye wathu! Tipangeni ife kukhala okumverani Inu ndi ana athu kukhala mtundu 2:128 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:128) ayat 128 in Chichewa

2:128 Surah Al-Baqarah ayat 128 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 128 - البَقَرَة - Page - Juz 1

﴿رَبَّنَا وَٱجۡعَلۡنَا مُسۡلِمَيۡنِ لَكَ وَمِن ذُرِّيَّتِنَآ أُمَّةٗ مُّسۡلِمَةٗ لَّكَ وَأَرِنَا مَنَاسِكَنَا وَتُبۡ عَلَيۡنَآۖ إِنَّكَ أَنتَ ٱلتَّوَّابُ ٱلرَّحِيمُ ﴾
[البَقَرَة: 128]

“Ambuye wathu! Tipangeni ife kukhala okumverani Inu ndi ana athu kukhala mtundu umene udzakumverani Inu ndipo tiphunzitseni miyambo yathu yopembedzera ndipo mutikhululukire. Ndithudi Inu ndinu okhululukira ndi Wachisoni chosatha.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ربنا واجعلنا مسلمين لك ومن ذريتنا أمة مسلمة لك وأرنا مناسكنا وتب, باللغة نيانجا

﴿ربنا واجعلنا مسلمين لك ومن ذريتنا أمة مسلمة لك وأرنا مناسكنا وتب﴾ [البَقَرَة: 128]

Khaled Ibrahim Betala
““E Mbuye wathu! Tichiteni Kukhalala Asilamu (ogonjera Inu), pamodzinso ndi ana athu muwachite kukhala fuko la Chisilamu (logonjera Inu). Ndipo tidziwitseni (njira) za mapemphero athu; ndipo landirani kulapa kwathu, ndithudi, Inu Ndinu Wolandira kulapa mochuluka; Wachisoni chosatha.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek