×

Iye ndiye amene adakulengerani inu zinthu zonse zimene zili padziko lapansi. Ndipo 2:29 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:29) ayat 29 in Chichewa

2:29 Surah Al-Baqarah ayat 29 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 29 - البَقَرَة - Page - Juz 1

﴿هُوَ ٱلَّذِي خَلَقَ لَكُم مَّا فِي ٱلۡأَرۡضِ جَمِيعٗا ثُمَّ ٱسۡتَوَىٰٓ إِلَى ٱلسَّمَآءِ فَسَوَّىٰهُنَّ سَبۡعَ سَمَٰوَٰتٖۚ وَهُوَ بِكُلِّ شَيۡءٍ عَلِيمٞ ﴾
[البَقَرَة: 29]

Iye ndiye amene adakulengerani inu zinthu zonse zimene zili padziko lapansi. Ndipo atatero analenga kumwamba ndipo adalenga miyamba isanu ndi iwiri ndipo Iye ndi wodziwa chinthu china chilichonse

❮ Previous Next ❯

ترجمة: هو الذي خلق لكم ما في الأرض جميعا ثم استوى إلى السماء, باللغة نيانجا

﴿هو الذي خلق لكم ما في الأرض جميعا ثم استوى إلى السماء﴾ [البَقَرَة: 29]

Khaled Ibrahim Betala
“Iye ndi Yemwe adakulengerani zonse za m’dziko lapansi, kenako adalunjika ku thambo nakonza thambo zisanu ndi ziwiri. Iye Ngodziwa chinthu chilichonse
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek