×

Ndipo Ife tidakwaniritsa lonjezo lathu kwa iwo, ndipo tidawapulumutsa iwo pamodzi ndi 21:9 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Anbiya’ ⮕ (21:9) ayat 9 in Chichewa

21:9 Surah Al-Anbiya’ ayat 9 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Anbiya’ ayat 9 - الأنبيَاء - Page - Juz 17

﴿ثُمَّ صَدَقۡنَٰهُمُ ٱلۡوَعۡدَ فَأَنجَيۡنَٰهُمۡ وَمَن نَّشَآءُ وَأَهۡلَكۡنَا ٱلۡمُسۡرِفِينَ ﴾
[الأنبيَاء: 9]

Ndipo Ife tidakwaniritsa lonjezo lathu kwa iwo, ndipo tidawapulumutsa iwo pamodzi ndi ena amene Ife tidawafuna koma tidaonongeratu anthu onse ochimwa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ثم صدقناهم الوعد فأنجيناهم ومن نشاء وأهلكنا المسرفين, باللغة نيانجا

﴿ثم صدقناهم الوعد فأنجيناهم ومن نشاء وأهلكنا المسرفين﴾ [الأنبيَاء: 9]

Khaled Ibrahim Betala
“Kenako tidawatsimikizira lonjezo (la kuwathangata pa adani awo), ndipo tidawapulumutsa iwo ndi amene tidawafuna (mwa omwe adawatsata), ndipo olumpha malire (a Allah) Tidawaononga
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek