×

M’nyama namonso muli chizindikiro choonetsa mphamvu zathu. Inu timakumwetsani zimene zili m’mimba 23:21 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Mu’minun ⮕ (23:21) ayat 21 in Chichewa

23:21 Surah Al-Mu’minun ayat 21 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Mu’minun ayat 21 - المؤمنُون - Page - Juz 18

﴿وَإِنَّ لَكُمۡ فِي ٱلۡأَنۡعَٰمِ لَعِبۡرَةٗۖ نُّسۡقِيكُم مِّمَّا فِي بُطُونِهَا وَلَكُمۡ فِيهَا مَنَٰفِعُ كَثِيرَةٞ وَمِنۡهَا تَأۡكُلُونَ ﴾
[المؤمنُون: 21]

M’nyama namonso muli chizindikiro choonetsa mphamvu zathu. Inu timakumwetsani zimene zili m’mimba mwake ndipo mumadya nyama yake ndiponso mumapeza phindu lambiri

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإن لكم في الأنعام لعبرة نسقيكم مما في بطونها ولكم فيها منافع, باللغة نيانجا

﴿وإن لكم في الأنعام لعبرة نسقيكم مما في بطونها ولكم فيها منافع﴾ [المؤمنُون: 21]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo ndithu m’ziweto muli lingaliro kwa inu. Timakumwetsani zomwe zili m’mimba mwake; ndipo m’zimenezo mukupeza zothandiza zambiri; ndipo zina mwa izo mumadya
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek