Quran with Chichewa translation - Surah An-Naml ayat 64 - النَّمل - Page - Juz 20
﴿أَمَّن يَبۡدَؤُاْ ٱلۡخَلۡقَ ثُمَّ يُعِيدُهُۥ وَمَن يَرۡزُقُكُم مِّنَ ٱلسَّمَآءِ وَٱلۡأَرۡضِۗ أَءِلَٰهٞ مَّعَ ٱللَّهِۚ قُلۡ هَاتُواْ بُرۡهَٰنَكُمۡ إِن كُنتُمۡ صَٰدِقِينَ ﴾
[النَّمل: 64]
﴿أمن يبدأ الخلق ثم يعيده ومن يرزقكم من السماء والأرض أإله مع﴾ [النَّمل: 64]
Khaled Ibrahim Betala “Kapena (wabwino) ndiamene adayambitsa zolengedwa, (ndipo) kenako adzazibweza, kapenanso amene amakupatsani rizq (chakudya) kuchokera kumwamba ndi m’nthaka? Kodi pamodzi ndi Allah pali mulungu winanso? Nena: “Bweretsani umboni wanu ngati mukunena zoona (wotsimikizira kuti Allah ali ndi mnzake).” |