Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qasas ayat 3 - القَصَص - Page - Juz 20
﴿نَتۡلُواْ عَلَيۡكَ مِن نَّبَإِ مُوسَىٰ وَفِرۡعَوۡنَ بِٱلۡحَقِّ لِقَوۡمٖ يُؤۡمِنُونَ ﴾
[القَصَص: 3]
﴿نتلوا عليك من نبإ موسى وفرعون بالحق لقوم يؤمنون﴾ [القَصَص: 3]
Khaled Ibrahim Betala “Tikukulakatulira (iwe Mtumiki) nkhani za Mûsa ndi Farawo m’njira yoona kwa anthu okhulupirira. (Koma osakhulupirira sangapindule kanthu ndi nkhanizi) |