×

Ndithudi Farawo adadzikweza pa dziko lapansi ndipo adagawa anthu ake m’magulumagulu ndipo 28:4 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Qasas ⮕ (28:4) ayat 4 in Chichewa

28:4 Surah Al-Qasas ayat 4 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qasas ayat 4 - القَصَص - Page - Juz 20

﴿إِنَّ فِرۡعَوۡنَ عَلَا فِي ٱلۡأَرۡضِ وَجَعَلَ أَهۡلَهَا شِيَعٗا يَسۡتَضۡعِفُ طَآئِفَةٗ مِّنۡهُمۡ يُذَبِّحُ أَبۡنَآءَهُمۡ وَيَسۡتَحۡيِۦ نِسَآءَهُمۡۚ إِنَّهُۥ كَانَ مِنَ ٱلۡمُفۡسِدِينَ ﴾
[القَصَص: 4]

Ndithudi Farawo adadzikweza pa dziko lapansi ndipo adagawa anthu ake m’magulumagulu ndipo gulu lina iye anali kulizunza pomapha ana awo aamuna ndi kusiya ana aakazi. Ndithudi iye adali wochita zoipa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إن فرعون علا في الأرض وجعل أهلها شيعا يستضعف طائفة منهم يذبح, باللغة نيانجا

﴿إن فرعون علا في الأرض وجعل أهلها شيعا يستضعف طائفة منهم يذبح﴾ [القَصَص: 4]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithu Farawo adadzikuza pa dziko, ndipo adawakhazika (anthu a m’dzikolo) m’magulumagulu; gulu lina la mwa iwo adalifooketsa (poliyesa akapolo) ndi kupha ana awo achimuna, ndi kuwasiya a moyo ana awo achikazi. Ndithu iye adali mmodzi wa oononga kwambiri
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek