Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qasas ayat 69 - القَصَص - Page - Juz 20
﴿وَرَبُّكَ يَعۡلَمُ مَا تُكِنُّ صُدُورُهُمۡ وَمَا يُعۡلِنُونَ ﴾
[القَصَص: 69]
﴿وربك يعلم ما تكن صدورهم وما يعلنون﴾ [القَصَص: 69]
Khaled Ibrahim Betala “Ndiponso Mbuye wako akudziwa zimene zifuwa zawo zikubisa (maganizo awo) ndi zimene akuwonetsera (poyera) |