Quran with Chichewa translation - Surah Ar-Rum ayat 14 - الرُّوم - Page - Juz 21
﴿وَيَوۡمَ تَقُومُ ٱلسَّاعَةُ يَوۡمَئِذٖ يَتَفَرَّقُونَ ﴾
[الرُّوم: 14]
﴿ويوم تقوم الساعة يومئذ يتفرقون﴾ [الرُّوم: 14]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo tsiku limene nthawi ya chiweruziro (Qiyâma) idzakwana, tsiku limenelo adzalekana (ena kukalowa ku Munda wamtendere, pomwe ena akalowa ku Moto) |