×

Ndipo aliyense wa inu amene ndi omvera Mulungu ndi Mtumwi wake ndipo 33:31 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ahzab ⮕ (33:31) ayat 31 in Chichewa

33:31 Surah Al-Ahzab ayat 31 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ahzab ayat 31 - الأحزَاب - Page - Juz 22

﴿۞ وَمَن يَقۡنُتۡ مِنكُنَّ لِلَّهِ وَرَسُولِهِۦ وَتَعۡمَلۡ صَٰلِحٗا نُّؤۡتِهَآ أَجۡرَهَا مَرَّتَيۡنِ وَأَعۡتَدۡنَا لَهَا رِزۡقٗا كَرِيمٗا ﴾
[الأحزَاب: 31]

Ndipo aliyense wa inu amene ndi omvera Mulungu ndi Mtumwi wake ndipo amachita ntchito zabwino, Ife tidzamupatsa malipiro ake kawiri ndipo tamukonzera iye chakudya cholemekezeka

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ومن يقنت منكن لله ورسوله وتعمل صالحا نؤتها أجرها مرتين وأعتدنا لها, باللغة نيانجا

﴿ومن يقنت منكن لله ورسوله وتعمل صالحا نؤتها أجرها مرتين وأعتدنا لها﴾ [الأحزَاب: 31]

Khaled Ibrahim Betala
“۞ Koma yense mwa inu amene amvere Allah ndi Mneneri Wake, ndi kumachita zabwino, timpatsa malipiro ake kawiri ndi kumkonzera rizq laulemu
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek