×

Ndithudi a Chisilamu amene amakhulupirira ndi amuna ndi akazi okhulupirira, amuna ndi 33:35 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ahzab ⮕ (33:35) ayat 35 in Chichewa

33:35 Surah Al-Ahzab ayat 35 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ahzab ayat 35 - الأحزَاب - Page - Juz 22

﴿إِنَّ ٱلۡمُسۡلِمِينَ وَٱلۡمُسۡلِمَٰتِ وَٱلۡمُؤۡمِنِينَ وَٱلۡمُؤۡمِنَٰتِ وَٱلۡقَٰنِتِينَ وَٱلۡقَٰنِتَٰتِ وَٱلصَّٰدِقِينَ وَٱلصَّٰدِقَٰتِ وَٱلصَّٰبِرِينَ وَٱلصَّٰبِرَٰتِ وَٱلۡخَٰشِعِينَ وَٱلۡخَٰشِعَٰتِ وَٱلۡمُتَصَدِّقِينَ وَٱلۡمُتَصَدِّقَٰتِ وَٱلصَّٰٓئِمِينَ وَٱلصَّٰٓئِمَٰتِ وَٱلۡحَٰفِظِينَ فُرُوجَهُمۡ وَٱلۡحَٰفِظَٰتِ وَٱلذَّٰكِرِينَ ٱللَّهَ كَثِيرٗا وَٱلذَّٰكِرَٰتِ أَعَدَّ ٱللَّهُ لَهُم مَّغۡفِرَةٗ وَأَجۡرًا عَظِيمٗا ﴾
[الأحزَاب: 35]

Ndithudi a Chisilamu amene amakhulupirira ndi amuna ndi akazi okhulupirira, amuna ndi akazi a chilungamo, amuna ndi akazi opirira, amuna ndi akazi ofatsa, amuna ndi akazi othandiza osauka, amuna ndi akazi osala, ndi amuna ndi akazi osachita chiwerewere ndi amuna ndi akazi amene amakumbukira Mulungu kwambiri; kwa anthu onse otere, Mulungu wawakonzera chikhululukiro ndi mphotho yaikulu

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إن المسلمين والمسلمات والمؤمنين والمؤمنات والقانتين والقانتات والصادقين والصادقات والصابرين والصابرات والخاشعين, باللغة نيانجا

﴿إن المسلمين والمسلمات والمؤمنين والمؤمنات والقانتين والقانتات والصادقين والصادقات والصابرين والصابرات والخاشعين﴾ [الأحزَاب: 35]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithu Asilamu achimuna ndi Asilamu achikazi; okhulupirira achimuna ndi okhulupirira achikazi; omvera achimuna ndi omvera achikazi; owona achimuna ndi owona achikazi; opirira achimuna ndi opirira achikazi; odzichepetsa achimuna ndi odzichepetsa achikazi; opereka sadaka achimuna ndi opereka sadaka achikazi; osala achimuna ndi osala achikazi; osunga umaliseche wawo (kuchiwerewere) achimuna ndi osunga umaliseche wawo achikazi; otamanda Allah kwambiri achimuna ndi otamanda Allah kwambiri achikazi, Allah wawakonzera chikhululuko ndi malipiro aakulu
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek