Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ahzab ayat 34 - الأحزَاب - Page - Juz 22
﴿وَٱذۡكُرۡنَ مَا يُتۡلَىٰ فِي بُيُوتِكُنَّ مِنۡ ءَايَٰتِ ٱللَّهِ وَٱلۡحِكۡمَةِۚ إِنَّ ٱللَّهَ كَانَ لَطِيفًا خَبِيرًا ﴾
[الأحزَاب: 34]
﴿واذكرن ما يتلى في بيوتكن من آيات الله والحكمة إن الله كان﴾ [الأحزَاب: 34]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo lowezani pamtima zimene zikunenedwa m’nyumba zanu; ndime za mawu a Allah ndi (zonena za Mtumiki) zanzeru. Ndithu Allah Ngodziwa zinthu zobisika kwambiri, ndi zapoyera |