Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ahzab ayat 46 - الأحزَاب - Page - Juz 22
﴿وَدَاعِيًا إِلَى ٱللَّهِ بِإِذۡنِهِۦ وَسِرَاجٗا مُّنِيرٗا ﴾
[الأحزَاب: 46]
﴿وداعيا إلى الله بإذنه وسراجا منيرا﴾ [الأحزَاب: 46]
Khaled Ibrahim Betala “Ndi kuti ukhale woitanira (anthu) kwa Allah kupyolera m’chifuniro Chake. Ndi (kutinso ukhale) nyali younikira (anthu) |