Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ahzab ayat 45 - الأحزَاب - Page - Juz 22
﴿يَٰٓأَيُّهَا ٱلنَّبِيُّ إِنَّآ أَرۡسَلۡنَٰكَ شَٰهِدٗا وَمُبَشِّرٗا وَنَذِيرٗا ﴾
[الأحزَاب: 45]
﴿ياأيها النبي إنا أرسلناك شاهدا ومبشرا ونذيرا﴾ [الأحزَاب: 45]
Khaled Ibrahim Betala “E iwe Mneneri (wa Allah)! Ndithu Ife takutuma (kuti ukhale) mboni (pa anthu ako ndi pa mibadwo yonse). Wonena nkhani zabwino (kwa oopa Allah), ndi mchenjezi (kwa onyoza Allah) |