Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ahzab ayat 63 - الأحزَاب - Page - Juz 22
﴿يَسۡـَٔلُكَ ٱلنَّاسُ عَنِ ٱلسَّاعَةِۖ قُلۡ إِنَّمَا عِلۡمُهَا عِندَ ٱللَّهِۚ وَمَا يُدۡرِيكَ لَعَلَّ ٱلسَّاعَةَ تَكُونُ قَرِيبًا ﴾
[الأحزَاب: 63]
﴿يسألك الناس عن الساعة قل إنما علمها عند الله وما يدريك لعل﴾ [الأحزَاب: 63]
Khaled Ibrahim Betala “Anthu akukufunsa za (kudza kwa) nthawi (ya tsiku la chitsiriziro). Nena: “Kuzindikira kwa nthawiyo kuli ndi Allah (Yekha). Nanga nchiyani chikudziwitse kuti nthawi ya chimaliziro iri pafupi?” |