Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ahzab ayat 70 - الأحزَاب - Page - Juz 22
﴿يَٰٓأَيُّهَا ٱلَّذِينَ ءَامَنُواْ ٱتَّقُواْ ٱللَّهَ وَقُولُواْ قَوۡلٗا سَدِيدٗا ﴾
[الأحزَاب: 70]
﴿ياأيها الذين آمنوا اتقوا الله وقولوا قولا سديدا﴾ [الأحزَاب: 70]
Khaled Ibrahim Betala “E inu amene mwakhulupirira! Opani Allah (pokwaniritsa malamulo Ake, ndi kusiya zoletsedwa), ndipo nenani mawu olungama |