×

Iye adzasunga ntchito zanu pamalo abwino ndi kukukhululukirani machimo anu. Ndipo aliyense 33:71 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ahzab ⮕ (33:71) ayat 71 in Chichewa

33:71 Surah Al-Ahzab ayat 71 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ahzab ayat 71 - الأحزَاب - Page - Juz 22

﴿يُصۡلِحۡ لَكُمۡ أَعۡمَٰلَكُمۡ وَيَغۡفِرۡ لَكُمۡ ذُنُوبَكُمۡۗ وَمَن يُطِعِ ٱللَّهَ وَرَسُولَهُۥ فَقَدۡ فَازَ فَوۡزًا عَظِيمًا ﴾
[الأحزَاب: 71]

Iye adzasunga ntchito zanu pamalo abwino ndi kukukhululukirani machimo anu. Ndipo aliyense amene amamvera Mulungu ndi Mtumwi wake, ndithudi, iyeyo wapeza chinthu chopambana

❮ Previous Next ❯

ترجمة: يصلح لكم أعمالكم ويغفر لكم ذنوبكم ومن يطع الله ورسوله فقد فاز, باللغة نيانجا

﴿يصلح لكم أعمالكم ويغفر لكم ذنوبكم ومن يطع الله ورسوله فقد فاز﴾ [الأحزَاب: 71]

Khaled Ibrahim Betala
“Akukonzerani bwino zochita zanu ndi kukukhululukirani machimo anu. ndipo amene akumvera Allah ndi Mtumiki Wake, ndithu apambana; kupambana kwakukulu
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek