×

oh inu anthu okhulupirira! Musakhale ngati anthu amene adayankhula zinthu zoipa zokhudza 33:69 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ahzab ⮕ (33:69) ayat 69 in Chichewa

33:69 Surah Al-Ahzab ayat 69 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ahzab ayat 69 - الأحزَاب - Page - Juz 22

﴿يَٰٓأَيُّهَا ٱلَّذِينَ ءَامَنُواْ لَا تَكُونُواْ كَٱلَّذِينَ ءَاذَوۡاْ مُوسَىٰ فَبَرَّأَهُ ٱللَّهُ مِمَّا قَالُواْۚ وَكَانَ عِندَ ٱللَّهِ وَجِيهٗا ﴾
[الأحزَاب: 69]

oh inu anthu okhulupirira! Musakhale ngati anthu amene adayankhula zinthu zoipa zokhudza Mose. Koma Mulungu adatsutsa zonse zimene anali kunena za Mose. Ndipo iye anali wolemekezeka kwa Mulungu

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ياأيها الذين آمنوا لا تكونوا كالذين آذوا موسى فبرأه الله مما قالوا, باللغة نيانجا

﴿ياأيها الذين آمنوا لا تكونوا كالذين آذوا موسى فبرأه الله مما قالوا﴾ [الأحزَاب: 69]

Khaled Ibrahim Betala
“E inu amene mwakhulupirira! Musakhale monga amene adamvutitsa Mûsa; koma Allah adamuyeretsa kuzimene ankamnenera. Ndipo iye kwa Allah adali wolemekezeka
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek