Quran with Chichewa translation - Surah As-saffat ayat 18 - الصَّافَات - Page - Juz 23
﴿قُلۡ نَعَمۡ وَأَنتُمۡ دَٰخِرُونَ ﴾
[الصَّافَات: 18]
﴿قل نعم وأنتم داخرون﴾ [الصَّافَات: 18]
Khaled Ibrahim Betala “Nena (iwe Mneneri): “Inde (mudzaukitsidwa inu pamodzi ndi makolo anu) uku inu muli onyozeka.” |