Quran with Chichewa translation - Surah As-saffat ayat 66 - الصَّافَات - Page - Juz 23
﴿فَإِنَّهُمۡ لَأٓكِلُونَ مِنۡهَا فَمَالِـُٔونَ مِنۡهَا ٱلۡبُطُونَ ﴾
[الصَّافَات: 66]
﴿فإنهم لآكلون منها فمالئون منها البطون﴾ [الصَّافَات: 66]
Khaled Ibrahim Betala “Ndithu iwo akadya mtengowo ndi kudzaza mimba zawo ndi zipatso zake (pakuti sakapeza chakudya china kupatula zipatso za mtengowo) |